Yoswa 19:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Malire a gawo lawo anakafika ku Yezereeli,+ Kesulotu, Sunemu,+ 1 Mafumu 18:45 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 45 Pa nthawiyo kumwamba kunachita mdima wa mitambo ndipo kunja kunawomba mphepo.+ Kenako kunayamba kugwa chimvula chambiri.+ Ahabu anali akuyenda pagaleta mpaka anakafika ku Yezereeli.+ Hoseya 2:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Ndiyeno dziko lapansi lidzayankha mbewu,+ vinyo wotsekemera ndi mafuta, ndipo zimenezi zidzayankha Yezereeli.*+
45 Pa nthawiyo kumwamba kunachita mdima wa mitambo ndipo kunja kunawomba mphepo.+ Kenako kunayamba kugwa chimvula chambiri.+ Ahabu anali akuyenda pagaleta mpaka anakafika ku Yezereeli.+
22 Ndiyeno dziko lapansi lidzayankha mbewu,+ vinyo wotsekemera ndi mafuta, ndipo zimenezi zidzayankha Yezereeli.*+