1 Samueli 12:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Choncho Samueli anafuulira Yehova,+ moti Yehova anadzetsa mabingu ndi mvula tsiku limenelo.+ Pamenepo anthu onse anachita mantha kwambiri ndi Yehova ndiponso ndi Samueli. Yobu 38:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Ndani amene ali ndi nzeru zoti angathe kudziwa chiwerengero cholondola cha mitambo,Kapena zosungira madzi akumwamba, ndani angathe kuzipendeketsa,+ Salimo 68:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Inu Mulungu, munayamba kugwetsa mvula yamphamvu,+Ngakhale pamene anthu anu anali ofooka, inu munawalimbitsa.+
18 Choncho Samueli anafuulira Yehova,+ moti Yehova anadzetsa mabingu ndi mvula tsiku limenelo.+ Pamenepo anthu onse anachita mantha kwambiri ndi Yehova ndiponso ndi Samueli.
37 Ndani amene ali ndi nzeru zoti angathe kudziwa chiwerengero cholondola cha mitambo,Kapena zosungira madzi akumwamba, ndani angathe kuzipendeketsa,+ Salimo 68:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Inu Mulungu, munayamba kugwetsa mvula yamphamvu,+Ngakhale pamene anthu anu anali ofooka, inu munawalimbitsa.+
9 Inu Mulungu, munayamba kugwetsa mvula yamphamvu,+Ngakhale pamene anthu anu anali ofooka, inu munawalimbitsa.+