Salimo 107:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Aona mmene amautsira mphepo yamkuntho mwa kungonena mawu,+Moti nyanjayo imachita mafunde.+ Salimo 147:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Amatumiza mawu ake+ ndi kusungunula madzi oundanawo.Amachititsa mphepo yake kuwomba,+Ndipo madzi amayenda. Yakobo 5:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Anapempheranso, ndipo mvula inagwa kuchokera kumwamba. Nthaka inatulutsa zipatso zake.+
18 Amatumiza mawu ake+ ndi kusungunula madzi oundanawo.Amachititsa mphepo yake kuwomba,+Ndipo madzi amayenda.