2 Mafumu 8:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 M’chaka cha 12 cha Yehoramu mwana wa Ahabu mfumu ya Isiraeli, Ahaziya mwana wa Yehoramu mfumu ya Yuda anakhala mfumu.+ 2 Mafumu 8:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Choncho mfumu Yehoramu+ inabwerera n’kupita ku Yezereeli+ kuti ikachire zilonda zimene Asiriya anaivulaza ku Rama,* pamene inali kumenyana ndi Hazaeli mfumu ya Siriya. Chotero Ahaziya+ mwana wa Yehoramu mfumu ya Yuda anapita ku Yezereeli kukaona Yehoramu mwana wa Ahabu chifukwa anali kudwala. 2 Mbiri 22:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Koma Mulungu ndi amene anachititsa+ kuti Ahaziya awonongeke+ mwa kupita kwa Yehoramu. Atafika kumeneko, anatengana+ ndi Yehoramu n’kupita kukakumana ndi Yehu+ mdzukulu wa Nimusi,+ yemwe Yehova anam’dzoza+ kuti aphe a m’nyumba ya Ahabu.+
25 M’chaka cha 12 cha Yehoramu mwana wa Ahabu mfumu ya Isiraeli, Ahaziya mwana wa Yehoramu mfumu ya Yuda anakhala mfumu.+
29 Choncho mfumu Yehoramu+ inabwerera n’kupita ku Yezereeli+ kuti ikachire zilonda zimene Asiriya anaivulaza ku Rama,* pamene inali kumenyana ndi Hazaeli mfumu ya Siriya. Chotero Ahaziya+ mwana wa Yehoramu mfumu ya Yuda anapita ku Yezereeli kukaona Yehoramu mwana wa Ahabu chifukwa anali kudwala.
7 Koma Mulungu ndi amene anachititsa+ kuti Ahaziya awonongeke+ mwa kupita kwa Yehoramu. Atafika kumeneko, anatengana+ ndi Yehoramu n’kupita kukakumana ndi Yehu+ mdzukulu wa Nimusi,+ yemwe Yehova anam’dzoza+ kuti aphe a m’nyumba ya Ahabu.+