2 Mafumu 9:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ukaphe anthu a m’nyumba ya mbuye wako Ahabu, kuti ine ndibwezere+ magazi a atumiki anga aneneri ndiponso magazi a atumiki onse a Yehova amene Yezebeli anapha.+
7 Ukaphe anthu a m’nyumba ya mbuye wako Ahabu, kuti ine ndibwezere+ magazi a atumiki anga aneneri ndiponso magazi a atumiki onse a Yehova amene Yezebeli anapha.+