1 Mafumu 19:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Ukadzozenso Yehu+ mdzukulu wa Nimusi+ kuti akhale mfumu ya Isiraeli, ndipo Elisa+ mwana wa Safati wa ku Abele-mehola,+ ukam’dzoze kuti akhale mneneri m’malo mwa iwe.+ 2 Mafumu 9:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Mlonda wa pansanja uja ananenanso kuti: “Munthu tamutuma ujanso wakumana nawo, koma sakubwerera. Ndipo mmene anthuwo akuthamangira, akuthamanga ngati Yehu+ mdzukulu wa Nimusi,+ pakuti iye amathamangitsa galeta ngati wamisala.”+
16 Ukadzozenso Yehu+ mdzukulu wa Nimusi+ kuti akhale mfumu ya Isiraeli, ndipo Elisa+ mwana wa Safati wa ku Abele-mehola,+ ukam’dzoze kuti akhale mneneri m’malo mwa iwe.+
20 Mlonda wa pansanja uja ananenanso kuti: “Munthu tamutuma ujanso wakumana nawo, koma sakubwerera. Ndipo mmene anthuwo akuthamangira, akuthamanga ngati Yehu+ mdzukulu wa Nimusi,+ pakuti iye amathamangitsa galeta ngati wamisala.”+