2 Mafumu 9:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ukakalowa mumzindawo, ukafufuze Yehu+ mwana wa Yehosafati mwana wa Nimusi. Ukakam’peza, ukamutenge pakati pa abale ake ndipo ukalowe naye m’chipinda chamkati.+ 2 Mafumu 9:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Kenako Yehu anafika ku Yezereeli,+ ndipo Yezebeli+ anamva zimenezo. Yezebeliyo anadzikongoletsa podzipaka utoto+ wakuda m’maso mwake n’kukongoletsanso tsitsi lake mochititsa kaso.+ Atatero anakaima pawindo n’kumayang’ana kunja.+
2 Ukakalowa mumzindawo, ukafufuze Yehu+ mwana wa Yehosafati mwana wa Nimusi. Ukakam’peza, ukamutenge pakati pa abale ake ndipo ukalowe naye m’chipinda chamkati.+
30 Kenako Yehu anafika ku Yezereeli,+ ndipo Yezebeli+ anamva zimenezo. Yezebeliyo anadzikongoletsa podzipaka utoto+ wakuda m’maso mwake n’kukongoletsanso tsitsi lake mochititsa kaso.+ Atatero anakaima pawindo n’kumayang’ana kunja.+