1 Mafumu 20:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Anthu amene anatsala anathawira kumzinda wa Afeki,+ ndipo khoma linagwera amuna 27,000 amene anatsala.+ Beni-hadadi anathawa+ ndipo pomalizira pake anafika mumzindawo n’kulowa m’chipinda chamkati.+ 1 Mafumu 22:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Pamenepo Mikaya anati: “Udzadziwa zimenezo tsiku limene udzalowe m’chipinda chamkati+ kukabisala.”+
30 Anthu amene anatsala anathawira kumzinda wa Afeki,+ ndipo khoma linagwera amuna 27,000 amene anatsala.+ Beni-hadadi anathawa+ ndipo pomalizira pake anafika mumzindawo n’kulowa m’chipinda chamkati.+
25 Pamenepo Mikaya anati: “Udzadziwa zimenezo tsiku limene udzalowe m’chipinda chamkati+ kukabisala.”+