Yesaya 3:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 M’tsiku limenelo Yehova adzachotsa zokongoletsera zawo zonse: zibangili za m’miyendo, zinthu zomanga kumutu, zodzikongoletsera zooneka ngati mwezi,+ 1 Petulo 3:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ndipo kudzikongoletsa kwanu kusakhale kwakunja, monga kumanga tsitsi,+ kuvala zodzikongoletsera zagolide,+ kapena kuvala malaya ovala pamwamba.
18 M’tsiku limenelo Yehova adzachotsa zokongoletsera zawo zonse: zibangili za m’miyendo, zinthu zomanga kumutu, zodzikongoletsera zooneka ngati mwezi,+
3 Ndipo kudzikongoletsa kwanu kusakhale kwakunja, monga kumanga tsitsi,+ kuvala zodzikongoletsera zagolide,+ kapena kuvala malaya ovala pamwamba.