2 Mafumu 9:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Tsopano Yehu+ mwana wa Yehosafati mwana wa Nimusi,+ anayamba kukonzera Yehoramu chiwembu.+ Pa nthawiyi n’kuti Yehoramu akulondera Ramoti-giliyadi+ pamodzi ndi Aisiraeli onse, chifukwa cha Hazaeli+ mfumu ya Siriya.
14 Tsopano Yehu+ mwana wa Yehosafati mwana wa Nimusi,+ anayamba kukonzera Yehoramu chiwembu.+ Pa nthawiyi n’kuti Yehoramu akulondera Ramoti-giliyadi+ pamodzi ndi Aisiraeli onse, chifukwa cha Hazaeli+ mfumu ya Siriya.