1 Mafumu 19:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Ukadzozenso Yehu+ mdzukulu wa Nimusi+ kuti akhale mfumu ya Isiraeli, ndipo Elisa+ mwana wa Safati wa ku Abele-mehola,+ ukam’dzoze kuti akhale mneneri m’malo mwa iwe.+
16 Ukadzozenso Yehu+ mdzukulu wa Nimusi+ kuti akhale mfumu ya Isiraeli, ndipo Elisa+ mwana wa Safati wa ku Abele-mehola,+ ukam’dzoze kuti akhale mneneri m’malo mwa iwe.+