2 Mafumu 10:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 M’mawa kutacha, Yehu anapita kukaima pamaso pa anthu onse. Kenako ananena kuti: “Anthu inu ndinu olungama.+ Ine ndinachitira chiwembu+ mbuye wanga, ndipo ndamupha,+ koma ndani wapha anthu onsewa?
9 M’mawa kutacha, Yehu anapita kukaima pamaso pa anthu onse. Kenako ananena kuti: “Anthu inu ndinu olungama.+ Ine ndinachitira chiwembu+ mbuye wanga, ndipo ndamupha,+ koma ndani wapha anthu onsewa?