2 Mafumu 9:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Pamenepo Yehu anakoka uta+ wake n’kulasa Yehoramu kumsana pakati pamapewa, mpaka muviwo unatulukira pamtima pake, moti Yehoramu anagwa m’galeta lake lankhondo.+
24 Pamenepo Yehu anakoka uta+ wake n’kulasa Yehoramu kumsana pakati pamapewa, mpaka muviwo unatulukira pamtima pake, moti Yehoramu anagwa m’galeta lake lankhondo.+