2 Mafumu 9:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ukakalowa mumzindawo, ukafufuze Yehu+ mwana wa Yehosafati mwana wa Nimusi. Ukakam’peza, ukamutenge pakati pa abale ake ndipo ukalowe naye m’chipinda chamkati.+
2 Ukakalowa mumzindawo, ukafufuze Yehu+ mwana wa Yehosafati mwana wa Nimusi. Ukakam’peza, ukamutenge pakati pa abale ake ndipo ukalowe naye m’chipinda chamkati.+