2 Mbiri 22:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Koma Mulungu ndi amene anachititsa kuti Ahaziya apite kwa Yehoramu kuti akaphedwe. Atafika kumeneko, anatengana ndi Yehoramu nʼkupita kukakumana ndi Yehu+ mdzukulu* wa Nimusi, amene Yehova anamudzoza kuti aphe anthu a mʼbanja la Ahabu.+
7 Koma Mulungu ndi amene anachititsa kuti Ahaziya apite kwa Yehoramu kuti akaphedwe. Atafika kumeneko, anatengana ndi Yehoramu nʼkupita kukakumana ndi Yehu+ mdzukulu* wa Nimusi, amene Yehova anamudzoza kuti aphe anthu a mʼbanja la Ahabu.+