Levitiko 26:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Iwo adzagwetsana okhaokha ngati kuti akuthawa lupanga, koma popanda munthu wowathamangitsa. Simudzatha n’komwe kulimbana ndi adani anu.+ Deuteronomo 32:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Kodi munthu mmodzi angathamangitse bwanji anthu 1,000,Kapena anthu awiri angapitikitse bwanji anthu 10,000?+ N’zosatheka, pokhapokha Thanthwe lawo litawagulitsa,+Komanso ngati Yehova atawapereka.
37 Iwo adzagwetsana okhaokha ngati kuti akuthawa lupanga, koma popanda munthu wowathamangitsa. Simudzatha n’komwe kulimbana ndi adani anu.+
30 Kodi munthu mmodzi angathamangitse bwanji anthu 1,000,Kapena anthu awiri angapitikitse bwanji anthu 10,000?+ N’zosatheka, pokhapokha Thanthwe lawo litawagulitsa,+Komanso ngati Yehova atawapereka.