2 Mafumu 14:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Mfumuyo itagona m’manda ndi makolo ake, Azariya anamanga mzinda wa Elati+ n’kuubwezera ku Yuda.