Deuteronomo 2:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Chotero tinalambalala abale athu, ana a Esau,+ amene akukhala m’Seiri, ndipo sitinayende njira ya Araba,+ Elati ndi Ezioni-geberi.+ “Kenako tinatembenuka ndi kudutsa njira ya m’chipululu cha Mowabu.+ 1 Mafumu 9:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Panali zombo zimene Mfumu Solomo inapanga ku Ezioni-geberi,+ pafupi ndi Eloti,+ pagombe la Nyanja Yofiira m’dziko la Edomu.+ 2 Mafumu 16:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Pa nthawiyo, Rezini mfumu ya Siriya anabwezeretsa mzinda wa Elati+ ku Edomu. Kenako anachotsa Ayuda mu Elati ndipo Aedomu analowa n’kumakhalamo. Iwo akukhalabe komweko mpaka lero. 2 Mbiri 26:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Mfumu itagona ndi makolo ake,+ Uziya anamanganso mzinda wa Eloti+ n’kuubwezeretsa ku Yuda.
8 Chotero tinalambalala abale athu, ana a Esau,+ amene akukhala m’Seiri, ndipo sitinayende njira ya Araba,+ Elati ndi Ezioni-geberi.+ “Kenako tinatembenuka ndi kudutsa njira ya m’chipululu cha Mowabu.+
26 Panali zombo zimene Mfumu Solomo inapanga ku Ezioni-geberi,+ pafupi ndi Eloti,+ pagombe la Nyanja Yofiira m’dziko la Edomu.+
6 Pa nthawiyo, Rezini mfumu ya Siriya anabwezeretsa mzinda wa Elati+ ku Edomu. Kenako anachotsa Ayuda mu Elati ndipo Aedomu analowa n’kumakhalamo. Iwo akukhalabe komweko mpaka lero.