Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Mafumu 9:26
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 Panali zombo zimene Mfumu Solomo inapanga ku Ezioni-geberi,+ pafupi ndi Eloti,+ pagombe la Nyanja Yofiira m’dziko la Edomu.+

  • 2 Mafumu 16:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Pa nthawiyo, Rezini mfumu ya Siriya anabwezeretsa mzinda wa Elati+ ku Edomu. Kenako anachotsa Ayuda mu Elati ndipo Aedomu analowa n’kumakhalamo. Iwo akukhalabe komweko mpaka lero.

  • 2 Mbiri 8:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Panali pa nthawi imeneyi pamene Solomo anapita ku Ezioni-geberi+ ndi ku Eloti,+ kugombe la nyanja m’dziko la Edomu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena