Yoswa 5:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ana a Isiraeliwo anakhalabe ku Giligala. Anachita pasika madzulo pa tsiku la 14 la mweziwo,+ ali m’chipululu cha Yeriko. Yoswa 9:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Kenako anapita kwa Yoswa kumsasa wa ku Giligala,+ ndipo anauza iye ndi amuna achiisiraeli kuti: “Ife tachokera kudziko lakutali kwambiri. Chonde, chitani nafe pangano.”+
10 Ana a Isiraeliwo anakhalabe ku Giligala. Anachita pasika madzulo pa tsiku la 14 la mweziwo,+ ali m’chipululu cha Yeriko.
6 Kenako anapita kwa Yoswa kumsasa wa ku Giligala,+ ndipo anauza iye ndi amuna achiisiraeli kuti: “Ife tachokera kudziko lakutali kwambiri. Chonde, chitani nafe pangano.”+