Yesaya 55:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Tcherani khutu+ lanu ndipo bwerani kwa ine.+ Mvetserani ndipo mudzakhalabe ndi moyo.+ Ine ndidzachita nanu pangano lokhalapo mpaka kalekale+ lokhudza kukoma mtima kwanga kosatha kosonyezedwa kwa Davide, kumene kuli kokhulupirika.+ Ezekieli 37:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 “‘“Ndidzachita nawo pangano la mtendere,+ moti adzakhala m’pangano limene lidzakhalepo mpaka kalekale.+ Ine ndidzawakhazikitsa m’dzikolo, ndidzawachulukitsa+ ndipo ndidzakhazikitsa malo anga opatulika pakati pawo mpaka kalekale.+
3 Tcherani khutu+ lanu ndipo bwerani kwa ine.+ Mvetserani ndipo mudzakhalabe ndi moyo.+ Ine ndidzachita nanu pangano lokhalapo mpaka kalekale+ lokhudza kukoma mtima kwanga kosatha kosonyezedwa kwa Davide, kumene kuli kokhulupirika.+
26 “‘“Ndidzachita nawo pangano la mtendere,+ moti adzakhala m’pangano limene lidzakhalepo mpaka kalekale.+ Ine ndidzawakhazikitsa m’dzikolo, ndidzawachulukitsa+ ndipo ndidzakhazikitsa malo anga opatulika pakati pawo mpaka kalekale.+