Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 33:28
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 28 Isiraeli adzakhala motetezeka,+

      Kasupe wa Yakobo adzakhala mosatekeseka,+

      M’dziko lokhala ndi chakudya ndi vinyo watsopano.+

      Ndipo kumwamba kwake kudzagwetsa mame.+

  • 1 Mafumu 4:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Ayuda+ ndi Aisiraeli anapitiriza kukhala mwabata.+ Aliyense anali pansi pa mtengo wake wa mpesa ndi mtengo wake wa mkuyu,+ kuchokera ku Dani mpaka ku Beere-seba,+ masiku onse a Solomo.

  • Salimo 4:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  8 Ndidzagona pansi ndi kupeza tulo mu mtendere,+

      Pakuti inu nokha Yehova mumandichititsa kukhala wotetezeka.+

  • Miyambo 1:33
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 33 Koma munthu wondimvera adzakhala mwabata+ ndipo sadzasokonezeka chifukwa choopa tsoka.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena