2 Mafumu 8:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Koma Yehova sanafune kuwononga ufumu wa Yuda+ chifukwa cha Davide mtumiki wake,+ pakuti anamulonjeza kuti adzam’patsa nyale+ nthawi zonse, iyeyo ndi ana ake.
19 Koma Yehova sanafune kuwononga ufumu wa Yuda+ chifukwa cha Davide mtumiki wake,+ pakuti anamulonjeza kuti adzam’patsa nyale+ nthawi zonse, iyeyo ndi ana ake.