2 Samueli 7:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Nyumba yako ndi ufumu wako zidzakhazikika pamaso pako mpaka kalekale. Mpando wako wachifumu udzakhazikika mpaka kalekale.”’”+ 2 Mbiri 21:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Koma Yehova sanafune kuwononga nyumba ya Davide+ chifukwa cha pangano+ limene anapangana ndi Davide, monga momwe anamuuzira kuti adzam’patsa+ nyale nthawi zonse, iyeyo ndi ana ake.+
16 Nyumba yako ndi ufumu wako zidzakhazikika pamaso pako mpaka kalekale. Mpando wako wachifumu udzakhazikika mpaka kalekale.”’”+
7 Koma Yehova sanafune kuwononga nyumba ya Davide+ chifukwa cha pangano+ limene anapangana ndi Davide, monga momwe anamuuzira kuti adzam’patsa+ nyale nthawi zonse, iyeyo ndi ana ake.+