1 Mafumu 11:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Mwana wake ndidzam’patsa fuko limodzi kuti Davide mtumiki wanga apitirize kukhala ndi nyale pamaso panga mu Yerusalemu,+ mzinda umene ndausankha kuti ndiikepo dzina langa.+ Salimo 132:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ku Ziyoniko ndidzakulitsa nyanga* ya Davide.+Wodzozedwa wanga ndamukonzera nyale.+ Luka 1:69 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 69 Iye watikwezera ife nyanga*+ yachipulumutso m’nyumba ya mtumiki wake Davide, Machitidwe 15:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 ‘Zimenezi zikadzatha ndidzabwerera ndi kumanganso nyumba ya Davide imene inagwa. Ndidzamanganso malo ogumuka a nyumbayo ndi kuiimikanso.+
36 Mwana wake ndidzam’patsa fuko limodzi kuti Davide mtumiki wanga apitirize kukhala ndi nyale pamaso panga mu Yerusalemu,+ mzinda umene ndausankha kuti ndiikepo dzina langa.+
16 ‘Zimenezi zikadzatha ndidzabwerera ndi kumanganso nyumba ya Davide imene inagwa. Ndidzamanganso malo ogumuka a nyumbayo ndi kuiimikanso.+