Amosi 9:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 “‘Pa tsiku limenelo, ndidzautsa+ nyumba+ ya Davide imene inagwa,+ ndi kukonza mmene khoma* lake linawonongeka. Ndidzautsa mabwinja ake ndipo ndidzaimanga kuti ikhale ngati masiku akale.+
11 “‘Pa tsiku limenelo, ndidzautsa+ nyumba+ ya Davide imene inagwa,+ ndi kukonza mmene khoma* lake linawonongeka. Ndidzautsa mabwinja ake ndipo ndidzaimanga kuti ikhale ngati masiku akale.+