2 Samueli 7:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 kuchokera tsiku limene ndinaika oweruza+ kuti azitsogolera anthu anga Aisiraeli. Ndidzakupatsa mpumulo kwa adani ako onse.+ “‘“Tsopano Yehova wakuuza kuti, Yehova adzakukhazikitsira banja lachifumu.+ Salimo 89:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Mbewu yake idzakhala mpaka kalekale,+Ndipo mpando wake wachifumu udzakhala ngati dzuwa pamaso panga.+
11 kuchokera tsiku limene ndinaika oweruza+ kuti azitsogolera anthu anga Aisiraeli. Ndidzakupatsa mpumulo kwa adani ako onse.+ “‘“Tsopano Yehova wakuuza kuti, Yehova adzakukhazikitsira banja lachifumu.+
36 Mbewu yake idzakhala mpaka kalekale,+Ndipo mpando wake wachifumu udzakhala ngati dzuwa pamaso panga.+