Salimo 103:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Tamanda Yehova, iwe moyo wanga,Ndipo usaiwale zochita zake zonse.+ Salimo 134:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 134 Tamandani Yehova,+Inu nonse atumiki a Yehova,+Inu amene mumaimirira m’nyumba ya Yehova usiku.+
2 Tamanda Yehova, iwe moyo wanga,Ndipo usaiwale zochita zake zonse.+ Salimo 134:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 134 Tamandani Yehova,+Inu nonse atumiki a Yehova,+Inu amene mumaimirira m’nyumba ya Yehova usiku.+