Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Levitiko 8:35
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 35 Chotero mukhale pakhomo la chihema chokumanako usana ndi usiku kwa masiku 7.+ Ndipo muyenera kuchita ulonda umene Yehova walamula,+ kuti musafe. Chifukwa n’zimene ndalamulidwa.”

  • 1 Mbiri 9:33
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 33 Amenewa ndiwo anali oimba,+ atsogoleri a makolo a Alevi m’zipinda zodyera.+ Iwo sanali kupatsidwa ntchito zina+ chifukwa usana ndi usiku anali ndi udindo wogwira ntchito yawo.+

  • Salimo 130:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  6 Ndayembekezera Yehova+

      Kuposa alonda amene akuyembekezera kuti kuche,+

      Ndithu kuposa alonda amene akuyembekezera kuti kuche.+

  • Luka 2:37
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 37 Tsopano anali mkazi wamasiye,+ ndipo anali ndi zaka 84 koma sanali kusowa pakachisi. Anali kuchita utumiki wopatulika usana ndi usiku,+ anali kusala kudya ndi kupereka mapembedzero.

  • Chivumbulutso 7:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 N’chifukwa chake ali pamaso+ pa mpando wachifumu wa Mulungu. Iwo akumuchitira utumiki wopatulika+ usana ndi usiku m’kachisi wake, ndipo wokhala pampando wachifumuyo+ adzatambasulira hema+ wake pamwamba pawo kuti awateteze.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena