Mateyu 4:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Koma Yesu anamuyankha kuti: “Choka Satana! Pakuti Malemba amati, ‘Yehova Mulungu wako ndi amene uyenera kumulambira,+ ndipo uyenera kutumikira+ iye yekha basi.’”+ Luka 2:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Tsopano anali mkazi wamasiye,+ ndipo anali ndi zaka 84 koma sanali kusowa pakachisi. Anali kuchita utumiki wopatulika usana ndi usiku,+ anali kusala kudya ndi kupereka mapembedzero.
10 Koma Yesu anamuyankha kuti: “Choka Satana! Pakuti Malemba amati, ‘Yehova Mulungu wako ndi amene uyenera kumulambira,+ ndipo uyenera kutumikira+ iye yekha basi.’”+
37 Tsopano anali mkazi wamasiye,+ ndipo anali ndi zaka 84 koma sanali kusowa pakachisi. Anali kuchita utumiki wopatulika usana ndi usiku,+ anali kusala kudya ndi kupereka mapembedzero.