1 Mbiri 23:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Analinso kutumikira m’mawa ulionse+ pa nthawi yoimirira+ kuti athokoze+ ndi kutamanda+ Yehova. Analinso kuchita zimenezi madzulo. Salimo 103:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Tamandani Yehova inu makamu ake onse,+Inu atumiki ake onse ochita chifuniro chake.+ Salimo 135:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Inu nyumba ya Isiraeli, tamandani Yehova.+Inu nyumba ya Aroni, tamandani Yehova.+ Luka 1:68 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 68 “Atamandike Yehova Mulungu wa Isiraeli,+ chifukwa wacheukira anthu ake+ ndi kuwapatsa chipulumutso.+ Yakobo 3:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Pakuti lilime timatamanda nalo Yehova,+ amenenso ndi Atate,+ komanso ndi lilime lomwelo timatemberera+ anthu amene analengedwa “m’chifaniziro cha Mulungu.”+
30 Analinso kutumikira m’mawa ulionse+ pa nthawi yoimirira+ kuti athokoze+ ndi kutamanda+ Yehova. Analinso kuchita zimenezi madzulo.
68 “Atamandike Yehova Mulungu wa Isiraeli,+ chifukwa wacheukira anthu ake+ ndi kuwapatsa chipulumutso.+
9 Pakuti lilime timatamanda nalo Yehova,+ amenenso ndi Atate,+ komanso ndi lilime lomwelo timatemberera+ anthu amene analengedwa “m’chifaniziro cha Mulungu.”+