Malaki 2:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 “Kodi tonsefe atate wathu si mmodzi?+ Kodi si Mulungu mmodzi amene anatilenga?+ N’chifukwa chiyani tikuchitirana zachinyengo,+ mwa kuipitsa pangano la makolo athu akale?+
10 “Kodi tonsefe atate wathu si mmodzi?+ Kodi si Mulungu mmodzi amene anatilenga?+ N’chifukwa chiyani tikuchitirana zachinyengo,+ mwa kuipitsa pangano la makolo athu akale?+