Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Mafumu 18:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Ngati amuna inu mungandiuze kuti, ‘Tikudalira+ Yehova Mulungu wathu,’+ kodi si iye amene Hezekiya+ wam’chotsera malo ake okwezeka+ ndi maguwa ake ansembe, n’kuuza Yuda ndi Yerusalemu kuti, ‘Muzigwada patsogolo pa guwa lansembe ili, la ku Yerusalemu’?”’+

  • 1 Mbiri 5:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Pa nkhondoyo iwo anathandizidwa moti Ahagara ndi onse amene anali nawo anaperekedwa m’manja mwawo, popeza anapempha Mulungu kuti awathandize+ ndipo iye anamva kupembedzera kwawo chifukwa anam’khulupirira.+

  • Aroma 9:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Iwo ndi ana a makolo akale aja.+ Komanso Khristu monga munthu,+ anatuluka pakati pawo. Mulungu,+ amene ndiye wamkulu pa zinthu zonse, atamandike kwamuyaya. Ame.

  • 1 Petulo 1:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Atamandike Mulungu amenenso ndi Atate wa Ambuye wathu Yesu Khristu,+ pakuti mwachifundo chake chachikulu, anatibereka mwatsopano+ kuti tikhale ndi chiyembekezo cha moyo+ mwa kuukitsidwa+ kwa Yesu Khristu.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena