1 Akorinto 15:44 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 44 Limafesedwa thupi lanyama,+ limaukitsidwa thupi lauzimu.+ Ngati pali thupi lanyama, palinso lauzimu. 1 Petulo 1:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Pakuti inu mwabadwa mwatsopano,+ osati kuchokera m’mbewu yotha kuwonongeka,+ koma m’mbewu+ yosatha kuwonongeka,+ kudzera m’mawu+ a Mulungu wamoyo ndi wamuyaya.+
44 Limafesedwa thupi lanyama,+ limaukitsidwa thupi lauzimu.+ Ngati pali thupi lanyama, palinso lauzimu.
23 Pakuti inu mwabadwa mwatsopano,+ osati kuchokera m’mbewu yotha kuwonongeka,+ koma m’mbewu+ yosatha kuwonongeka,+ kudzera m’mawu+ a Mulungu wamoyo ndi wamuyaya.+