1 Akorinto 6:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Chakudya ndi cha mimba, ndipo mimba ndi ya chakudya,+ koma Mulungu adzawononga mimba ndi chakudya chomwe.+ Choncho thupi silochitira dama koma ndi la Ambuye,+ ndipo Ambuye ndiye mwini thupi.+
13 Chakudya ndi cha mimba, ndipo mimba ndi ya chakudya,+ koma Mulungu adzawononga mimba ndi chakudya chomwe.+ Choncho thupi silochitira dama koma ndi la Ambuye,+ ndipo Ambuye ndiye mwini thupi.+