2 Mbiri 32:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Iyo ikudalira mphamvu za anthu,*+ koma ife tili ndi Yehova Mulungu wathu+ kuti atithandize ndi kutimenyera nkhondo zathu.”+ Pamenepo anthuwo anayamba kulimba mtima chifukwa cha mawu a Hezekiya mfumu ya Yuda.+
8 Iyo ikudalira mphamvu za anthu,*+ koma ife tili ndi Yehova Mulungu wathu+ kuti atithandize ndi kutimenyera nkhondo zathu.”+ Pamenepo anthuwo anayamba kulimba mtima chifukwa cha mawu a Hezekiya mfumu ya Yuda.+