Salimo 9:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Anthu odziwa dzina lanu adzakukhulupirirani,+Pakuti simudzasiya ndithu anthu okufunafunani, inu Yehova.+ Salimo 20:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ena akunena za magaleta* ndipo ena akunena za mahatchi,*+Koma ife tidzanena za dzina la Yehova Mulungu wathu.+ Salimo 22:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Makolo athu anali kudalira inu.+Iwo anali kudalira inu ndipo munali kuwapulumutsa.+ Aheberi 11:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Mwa chikhulupiriro, anthu amenewa anagonjetsa maufumu pa nkhondo,+ anachita chilungamo,+ analandira malonjezo+ ndiponso anatseka mikango pakamwa.+
10 Anthu odziwa dzina lanu adzakukhulupirirani,+Pakuti simudzasiya ndithu anthu okufunafunani, inu Yehova.+
7 Ena akunena za magaleta* ndipo ena akunena za mahatchi,*+Koma ife tidzanena za dzina la Yehova Mulungu wathu.+
33 Mwa chikhulupiriro, anthu amenewa anagonjetsa maufumu pa nkhondo,+ anachita chilungamo,+ analandira malonjezo+ ndiponso anatseka mikango pakamwa.+