Salimo 91:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Mulungu wanena kuti: “Popeza wasonyeza kuti amandikonda,+Inenso ndidzamupulumutsa.+Ndidzamuteteza chifukwa wadziwa dzina langa.+ Miyambo 18:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Dzina la Yehova ndi nsanja yolimba.+ Wolungama amathawira mmenemo ndipo amatetezedwa.+ Yeremiya 16:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 “Choncho ine ndiwaphunzitsa. Pa nthawi ino yokha ndiwaonetsa dzanja langa ndi mphamvu zanga,+ ndipo adziwa kuti dzina langa ndine Yehova.”+
14 Mulungu wanena kuti: “Popeza wasonyeza kuti amandikonda,+Inenso ndidzamupulumutsa.+Ndidzamuteteza chifukwa wadziwa dzina langa.+
21 “Choncho ine ndiwaphunzitsa. Pa nthawi ino yokha ndiwaonetsa dzanja langa ndi mphamvu zanga,+ ndipo adziwa kuti dzina langa ndine Yehova.”+