Ekisodo 15:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Yehova ndi wankhondo.+ Dzina lake ndi Yehova.+ Salimo 83:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Kuti anthu adziwe+ kuti inu, amene dzina lanu ndinu Yehova,+Inu nokha ndinu Wam’mwambamwamba,+ wolamulira dziko lonse lapansi.+ Yeremiya 33:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Yehova Wopanga+ dziko lapansi, Yehova Woumba+ dzikoli ndi kulikhazikitsa.+ Mulungu amene dzina lake ndi Yehova,+ wanena kuti,
18 Kuti anthu adziwe+ kuti inu, amene dzina lanu ndinu Yehova,+Inu nokha ndinu Wam’mwambamwamba,+ wolamulira dziko lonse lapansi.+
2 “Yehova Wopanga+ dziko lapansi, Yehova Woumba+ dzikoli ndi kulikhazikitsa.+ Mulungu amene dzina lake ndi Yehova,+ wanena kuti,