Salimo 96:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Nenani pakati pa anthu a mitundu ina kuti: “Yehova wakhala mfumu.+Dziko lapansi nalonso lakhazikika moti silingagwedezeke.+Iye adzaweruzira mitundu ya anthu milandu yawo mwachilungamo.”+ Salimo 104:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Mwakhazikitsa dziko lapansi pamaziko olimba.+Silidzagwedezeka mpaka kalekale, mpaka muyaya.+ Salimo 119:90 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 90 Kukhulupirika kwanu kudzakhalapobe ku mibadwomibadwo.+Mwakhazikitsa mwamphamvu dziko lapansi, kuti lisagwedezeke.+ Mlaliki 1:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 M’badwo umapita+ ndipo m’badwo wina umabwera,+ koma dziko lapansi lidzakhalapobe mpaka kalekale.*+
10 Nenani pakati pa anthu a mitundu ina kuti: “Yehova wakhala mfumu.+Dziko lapansi nalonso lakhazikika moti silingagwedezeke.+Iye adzaweruzira mitundu ya anthu milandu yawo mwachilungamo.”+
90 Kukhulupirika kwanu kudzakhalapobe ku mibadwomibadwo.+Mwakhazikitsa mwamphamvu dziko lapansi, kuti lisagwedezeke.+