Salimo 93:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 93 Yehova wakhala mfumu!+Iye wavala ulemerero.+Yehova wavala mphamvu ngati chovala, ndipo wamangirira mphamvuzo m’chiuno mwake.+Dziko lapansi lakhazikika, moti silingagwedezeke.+ Salimo 96:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Nenani pakati pa anthu a mitundu ina kuti: “Yehova wakhala mfumu.+Dziko lapansi nalonso lakhazikika moti silingagwedezeke.+Iye adzaweruzira mitundu ya anthu milandu yawo mwachilungamo.”+ Mlaliki 1:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 M’badwo umapita+ ndipo m’badwo wina umabwera,+ koma dziko lapansi lidzakhalapobe mpaka kalekale.*+
93 Yehova wakhala mfumu!+Iye wavala ulemerero.+Yehova wavala mphamvu ngati chovala, ndipo wamangirira mphamvuzo m’chiuno mwake.+Dziko lapansi lakhazikika, moti silingagwedezeke.+
10 Nenani pakati pa anthu a mitundu ina kuti: “Yehova wakhala mfumu.+Dziko lapansi nalonso lakhazikika moti silingagwedezeke.+Iye adzaweruzira mitundu ya anthu milandu yawo mwachilungamo.”+