Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 1:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Patapita nthawi Yosefe anamwalira.+ Ndipo abale ake onse ndi m’badwo wonsewo anamwaliranso.

  • Salimo 89:47
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 47 Kumbukirani utali wa moyo wanga.+

      Kodi ana onse a anthu munawalenga pachabe?+

  • Salimo 90:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Masiku a moyo wathu amangokwana zaka 70,+

      Ndipo ngati tili ndi mphamvu yapadera amakwana zaka 80.+

      Koma ngakhale zili choncho, amangodzaza ndi mavuto ndi zopweteka.+

      Pakuti masiku amene timakhala ndi moyo amatha mwamsanga ndipo timachoka mofulumira.+

  • Mlaliki 12:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Kenako fumbi lidzabwerera kunthaka+ kumene linali, ndipo mzimu*+ udzabwerera kwa Mulungu woona+ amene anaupereka.+

  • Zekariya 1:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 “‘Kodi makolo anuwo ali kuti?+ Ndipo “kodi aneneriwo+ anapitirizabe kukhala ndi moyo mpaka kalekale?”*

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena