Genesis 50:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Patapita nthawi, Yosefe anamwalira ali ndi zaka 110. Thupi lake analikonza ndi mankhwala kuti lisawonongeke,+ ndipo analiika m’bokosi ku Iguputoko.
26 Patapita nthawi, Yosefe anamwalira ali ndi zaka 110. Thupi lake analikonza ndi mankhwala kuti lisawonongeke,+ ndipo analiika m’bokosi ku Iguputoko.