Genesis 50:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Kenako Yosefe analamula atumiki ake omwe anali madokotala, kuti akonze mtembo wa bambo ake ndi mankhwala kuti usawonongeke.+ Choncho madokotalawo anakonza mtembo wa Isiraeli.
2 Kenako Yosefe analamula atumiki ake omwe anali madokotala, kuti akonze mtembo wa bambo ake ndi mankhwala kuti usawonongeke.+ Choncho madokotalawo anakonza mtembo wa Isiraeli.