Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yobu 14:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Koma mwamuna wamphamvu amafa ndipo amagona pansi atagonjetsedwa.

      Munthu wochokera kufumbi amatha. Kodi ali kuti?+

  • Salimo 78:39
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 39 Iye anali kukumbukira nthawi zonse kuti iwo ndi anthu athupi la nyama,+

      Anali kukumbukira kuti moyo wawo umachoka ndipo subwereranso.+

  • Luka 12:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Koma Mulungu anamuuza kuti, ‘Wopanda nzeru iwe, usiku womwe uno moyo wako adzaufuna.+ Nanga chuma chimene waunjikachi chidzakhala cha ndani?’+

  • Yakobo 4:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Mumatero chonsecho simukudziwa kuti moyo wanu udzakhala wotani mawa.+ Pakuti ndinu nkhungu yongoonekera kanthawi kenako n’kuzimiririka.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena