Yobu 7:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Kumbukirani kuti moyo wanga uli ngati mphepo,+Ndiponso kuti diso langa silidzaonanso zabwino. Salimo 39:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Taonani! Mwachepetsa masiku anga.+Ndipo nthawi ya moyo wanga si kanthu pamaso panu.+Ndithudi, munthu aliyense ngakhale atakhala wamphamvu bwanji, sali kanthu koma ali ngati mpweya wotuluka m’mphuno.+ [Seʹlah.] Salimo 119:84 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 84 Kodi ine mtumiki wanu ndidikira kufikira liti?+Kodi anthu ondizunza mudzawaweruza liti?+
5 Taonani! Mwachepetsa masiku anga.+Ndipo nthawi ya moyo wanga si kanthu pamaso panu.+Ndithudi, munthu aliyense ngakhale atakhala wamphamvu bwanji, sali kanthu koma ali ngati mpweya wotuluka m’mphuno.+ [Seʹlah.]