Salimo 119:84 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 84 Kodi ine mtumiki wanu ndidikira mpaka liti? Kodi anthu amene akundizunza mudzawaweruza liti?+