Salimo 119:84 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 84 Kodi ine mtumiki wanu ndidikira kufikira liti?+Kodi anthu ondizunza mudzawaweruza liti?+