Yobu 7:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Kumbukirani kuti moyo wanga uli ngati mphepo,+Ndiponso kuti diso langa silidzaonanso zabwino. Salimo 39:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 “Inu Yehova, ndidziwitseni za kufulumira kwa chimaliziro changa,+Ndiponso kuti masiku anga ndi ochepa motani,+Kuti ndidziwe kufupika kwa moyo wanga.+ Salimo 89:47 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 47 Kumbukirani utali wa moyo wanga.+Kodi ana onse a anthu munawalenga pachabe?+
4 “Inu Yehova, ndidziwitseni za kufulumira kwa chimaliziro changa,+Ndiponso kuti masiku anga ndi ochepa motani,+Kuti ndidziwe kufupika kwa moyo wanga.+