Yobu 14:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 “Munthu wobadwa kwa mkazi,+Amakhala ndi moyo waufupi,+ wodzaza ndi masautso.+ Salimo 144:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Munthu amafanana ndi mpweya wotuluka m’mphuno.+Masiku ake ali ngati mthunzi wongodutsa.+ Mlaliki 11:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ngakhale munthu atakhala ndi moyo zaka zambiri, m’zaka zonsezo azisangalala.+ Iye akumbukire masiku a mdima,+ ngakhale atakhala ambiri. Tsiku lililonse limene likubwera n’lachabechabe.+
8 Ngakhale munthu atakhala ndi moyo zaka zambiri, m’zaka zonsezo azisangalala.+ Iye akumbukire masiku a mdima,+ ngakhale atakhala ambiri. Tsiku lililonse limene likubwera n’lachabechabe.+